PATRICK PHIRI AKUFUNIKA
PETER MPONDA AKUFUNA PATRICK PHIRI
Mphunzitsi wa timu ya Master security Peter Mponda akufuna Patrick Phiri osewela wa Karonga United kuti akatumikile Masters FC season ikubwerayi phiri.
Patrick Phiri wasewelapo Mateam monga Surestream,FCB Nyasa Big Bullets komaso Civil service United.
Timu ya Masters Security yomwe yangobwelelanso kumene mu ligi yayikulu ya mziko muno, inakhulupilira zintchito Za Peter mponda kuti akhale Mphunzisi wankulu ku timuyi.
Pamene akulu akulu Amati akangalika kukomzekela ligi yachaka chino.Nawo aphunzisi amatimuwa ali pachintchito chosaka osewela apamwamba kuti awathandize mu mpikisano wachaka chino.
Wolemba: Steven Pangani
Kanema: Kuwonesa Patrick Phiri
Comments
Post a Comment