MALAMULO ASINTHA
FIFA YASINTHA ENA MWALAMULO WOYENDESELA MPIKISANO WADZIKO LONSE LAPANSI
Ndipo ena mwamalamulo atsopano amene adzagwiritsidwe ntchito ku World Cup ndi awa:
• VAR idzatha kuwunika khadi lachiwiri lachikaso (second yellow card) kapena corner kick ngati yaona kuti panali cholakwika.
• Wosewera akasinthidwa (substituted), adzakhala ndi masekondi 10 kuti atuluke pabwalo. Ngati atenga nthawi yaitali kuposa pamenepo, wosewera amene akulowa adzayenera kudikira mphindi imodzi asanalowe.
• Ngati wosewera wapempha chithandizo cha madokotala ali pabwalo, adzayenera kuchoka pabwalo kwa mphindi imodzi asanabwerere.
QMalamulo atsopano amene adzagwiritsidwe ntchito ku World Cup
• VAR idzatha kuwunika khadi lachiwiri lachikaso (second yellow card) kapena corner kick ngati yaona kuti panali cholakwika.
• Wosewera akasinthidwa (substituted), adzakhala ndi masekondi 10 kuti atuluke pabwalo. Ngati atenga nthawi yaitali kuposa pamenepo, wosewera amene akulowa adzayenera kudikira mphindi imodzi asanalowe.
• Ngati wosewera wapempha chithandizo cha madokotala ali pabwalo, adzayenera kuchoka pabwalo kwa mphindi imodzi asanabwerere.
• Ngati woweruza waona kuti pali kuchedwetsa nthawi pa throw-in kapena goal kick, kwa masekondi 5. Ngati mpira suikidwa m’masewera mkati mwa nthawi imeneyo, throw-in idzaperekedwa ku timu ina, ndipo pa goal kick izasintha kukhala corner kick kupita ku timu inayo.

Malamulowa ayamba kugwira Ntchito mu World Cup ikubwelayi
Wolemba: Steven Pangani
Source: Sports Touch
Video: Shows FIFA new rules
Comments
Post a Comment