AYITANIDWA KWA NTHAWI YOYAMBA
MAFAITI, KHUNGWA, WALLACE AYITANIDWA KU FLAMES
Mphunzitsi watimu ya dziko lino, Kalisto Pasuwa, wayitana 22 omwe alowe m'bindikiro kukonzekera masewero a matimu anayi ku Botswana kumathero a mwezi uno.
Mphunzitsiyu waitanako Charles Mafaiti wa Civil Service United koyamba ku m'bindikirowu monganso Alex Kambirinya, Hermas Masinja, Dan Sandukira ndi Festus Duwe.
Mpikisanowu udzayamba pa 23 March mpaka pa 31 March ndipo matimu a Botswana, Zimbabwe ndi Zambia ndi enanso omwe atenge nawo mbali.
Awa ndi osewela onse omwe ayitanidwa mu camp ya flames:
OTCHINGA PAGOLO
Dalitso Khungwa
George Chikooka
Joshua Waka
OTCHINGA KUMBUYO
Blessings Mpokera
Alex Kambirinya
Emmanuel Nyirenda
Fanizo Mwansambo
Hermus Masinja
Charles Mafaiti
Dan Sandukira
OSEWERA PAKATI
Yankho Singo
Moses Banda
Blessings Singini
Festus Duwe
Uchizi Vunga
Chawanangwa Gumbo
OMWETSA ZIGOLI
Andrew Joseph
Ephraim Kondowe
Allen Chihana
Gaddie Chirwa
Wolemba: Steven Pangani
Source: Football Association of Malawi
Video: Showing Malawi National football team preparations
Comments
Post a Comment