MWAMBO UWONESEDWA PA KANEMA
MWAMBO WOYIKA THUPI LA KANYENDA UWONESEDWA PA KANEMA.
Pamene thupi la amene ankasewera kutsogolo kwa timu ya Mighty Wanderers komanso Flames, Esau Black Mamba Kanyenda likuyembekezeka kulowa m'manda Lachitatu likubwerali, mabungwe a FAM ndi Football Legends ati apereka mwayi kwa a Malawi woowonela mwambowu pa kanema.
Izi ndi malingana ndikuti kanema wa mibawa watsimikiza Za izi pa tsamba lawo la nchezo la Facebook.
Kanyenda anamwalira pa 02 December, 2025 m'dziko la United Kingdom atadwala nthenda ya ipso.
Wolemba: Steven Pangani
Video: Showing performance of Kanyenda when he was alive.
He will be missed
ReplyDeleteSizinayende pamenepo 😌
ReplyDelete