MASAPOTA ATONTHOZA NYIRENDA

 ENA MWA MASAPOTA A TIMU YA MIGHTY WANDERERS ATONTHOZA EMMANUEL NYIRENDA.


Lero masapota a tsamba la mchezo la WhatsApp lotchedwa TRUE WANDERERS DIEHARD anamuyendera player wawo Emmanuel Nyirenda maka chifukwa chotaya Bambo ake masiku apitawa.

Masapotawa anapanga pang'ono pang'ono kukamupatsa Emmanuel ndi mawu achitonthozo komanso omulimbikitsa pamene akudutsa mu nyengo yowawitsayi.

Emmanuel wathokoza kwambiri ponena kuti sanayembekezere kuti Masapota angamayende naye munyengo ngati izizi. Ndipo wati izizi sizathere pa iye koma chikondichi chizipita kwa Player aliyense.

Wolemba: Steven Pangani 



Comments

Popular posts from this blog

MWAMBO UWONESEDWA PA KANEMA

ON THE WAY TO WOMEN FIFA U20

IRAN WITHDRAW FIFA WORLD CUP