KATSIRI WA NET WAYIMA KAYE
Katswiri wa mpira wa Manja mdziko muno Joyce Mvura walengedza kuti wasiya Kaye kusewera Masewero ndipo chidwi chake chalunjika posamalira banja lake.
Katswiri yu wathokoza Bungwe la Netball Association of Malawi , England Netball,omutsatira komanso ndi ena kamba ka Support yawo pa iye.
Mvura wati sikuti watheratu ayi kamba koti iye ndi wa Netball koma panopa wangoima Kaye.
Source: Grandmax Sports ports Update

Comments
Post a Comment