ADINDO A BULLETS AKUKONZEKELA

FCB NYASA BIG BULLETS IKUFUNA KULIMBISA TEAM NDI WOSEWELA ATSOPANO

Mphunzitsi wongogwilizira watimu ya FCB Nyasa Big Bullets, Gilbert Chirwa ndim'modzi mwa adindo omwe akukhudzidwa ndi ntchito yofunafuna osewera atsopano kutimuyi pofuna kukonzanso timuyi pokonzekera sizoni yatsopano. 

Pakadali pano, timuyi yamvana ndi osewera angapo kuphatikizapo goloboyi watimu ya Karonga United, McLean Mwale komanso George Chaomba wosewera kutsogolo watimu ya Creck Sporting Club.

Izi zikuza chifukwa team ya FCB Nyasa Big Bullets siidachite bwino kweni kweni season ino zomwe zidapangisa kuti achose mphuzisi wawo Steven Pangan. 

Wolemba: Steven Pangani 




Comments

Popular posts from this blog

MWAMBO UWONESEDWA PA KANEMA

ON THE WAY TO WOMEN FIFA U20

IRAN WITHDRAW FIFA WORLD CUP